Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 11:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndinali ine m'mudzi wa Yopa ndi kupemphera; ndipo m'kukomoka ndinaona masomphenya, cotengera cirikutsika, ngati cinsaru cacikuru cogwiridwa pa ngondya zace zinai; ndi kutsika kumwamba, ndipo cinadza pali ine;

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 11

Onani Macitidwe 11:5 nkhani