Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 11:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Koma atumwi ndi abale akukhala m'Yudeya anamva kuti amitundunso adalandira mau a Mulungu.

2. Ndipo pamene Petro adakwera kudza ku Yerusalemu, iwo a kumdulidwe anatsutsana naye,

3. nanena kuti, Munalowa kwa anthu osadulidwa, ndi kudya nao.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 11