Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 10:47-48 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

47. Kodi pali munthu akhoza kuletsa madzi, kuti asabatizidwe awa, amene alandira Mzimu Woyera 8 ngatinso ife?

48. Ndipo analamulira iwo 9 abatizidwe m'dzina la Yesu Kristu, Pamenepo anampempha iye atsotse masiku.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 10