Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 10:30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Komeliyo anati, Atapita masiku anai, kufikira monga ora ili, ndinalikupemphera m'nyumba yanga pa ora lacisanu ndi cinai; ndipo taonani, padaimirira pamaso panga munthu wobvala cobvala conyezimira,

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 10

Onani Macitidwe 10:30 nkhani