Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 10:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anati, Komeliyo kenturiyoyo, munthu wolungama ndi wakuopa Mulungu, amene mtundu wonse wa Ayuda umcitira umboni, anacenjezedwa ndi mngelo woyera kuti atumize nakuitaneni mumuke ku nyumba yace, ndi kummvetsa mau anu.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 10

Onani Macitidwe 10:22 nkhani