Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Macitidwe 10:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pokayika-kayika Petro mwa yekha ndi kuti masomphenya adawaona akuti ciani, taonani, amuna aja otumidwa ndi Komeliyo, atafunsira nyumba ya Simoni, anaima pa cipata,

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 10

Onani Macitidwe 10:17 nkhani