Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Luka 9:60-62 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

60. Koma anati kwa iye, Leka akufa aike akufa a eni okha; koma muka iwe nubukitse mbiri yace ya Ufumu wa Mulungu.

61. Ndipo winanso anati, Ambuye ndidzakutsatani Inu; koma muthange mwandilola kulawirana nao a kunyumba kwanga.

62. Koma Yesu anati kwa iye, Palibe munthu wakugwira cikhasu, nayang'ana za kumbuyo, ayenera Ufumu wa Mulungu.

Werengani mutu wathunthu Luka 9