Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Luka 9:33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo panali polekana iwo aja ndi iye, Petro anati kwa Yesu, Ambuye, nkwabwino kuti tiri pano; ndipo timange misasa itatu, umodzi wa Inu, ndi wina wa Mose, ndi wina wa Eliya; wosadziwa iye cimene alikunena.

Werengani mutu wathunthu Luka 9

Onani Luka 9:33 nkhani