Luka 8:52-54 Buku Lopatulika 1992 (BL92) Ndipo anthu onse analikumlira iye ndi kudzigugudapacifuwa. Koma iye anati, Musalire; pakuti iye sanafa, koma agona