Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Luka 8:35 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iwo anaturuka kukaona cimene cinacitika; ndipo anadza kwa Yesu, nampeza munthuyo, amene ziwanda zinaturuka mwa iye, alikukhala pansi ku mapazi ace a Yesu wobvala ndi wa nzeru zace; ndipo iwo anaopa.

Werengani mutu wathunthu Luka 8

Onani Luka 8:35 nkhani