Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Luka 8:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti iye adalamula mzimu wonyansa uturuke mwa munthuyo. Pakuti nthawi zambiri unamgwira; ndipo anthu anammanga ndi maunyolo ndi matangadza kumsungira; ndipo anamwetula zomangirazo, nathawitsidwa ndi ciwandaco kumapululu.

Werengani mutu wathunthu Luka 8

Onani Luka 8:29 nkhani