Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Luka 7:48-50 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

48. Ndipo anati kwa mkazi, Macimo ako akhululukidwa.

49. Ndipo iwo akuseama naye pacakudya anayamba kunena mwa okha, Uyu ndani amene akhululukiranso macimo?

50. Ndipo Iyeanati kwa mkaziyo, Cikhulupiriro cako cakupulumutsa iwe; muka ndi mtendere.

Werengani mutu wathunthu Luka 7