Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Luka 7:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anayankha, nati kwa iwo, Mukani, muuze Yohane zimene mwaziona, nimwazimva; anthu akhungu alandira kuona kwao, opunduka miyendo ayenda, akhate akonzedwa, ogontha akumva, akufa aukitsidwa, kwa aumphawi ulalikidwa Uthenga Wabwino.

Werengani mutu wathunthu Luka 7

Onani Luka 7:22 nkhani