Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Luka 7:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anayandikira, nakhudza cithatha; ndipo akumnyamulawo anaima. Ndipo iye anati, Mnyamata iwe, ndinena ndi iwe, Tauka.

Werengani mutu wathunthu Luka 7

Onani Luka 7:14 nkhani