Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Luka 7:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pamene anayandikira ku cipata ca mudziwo, onani, anthu analikunyamula munthu wakufa, mwana wamwamuna mmodzi yekha, amace ndiye mkazi wamasiye; ndipo anthu ambiri a kumudzi anali pamodzi naye.

Werengani mutu wathunthu Luka 7

Onani Luka 7:12 nkhani