Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Luka 6:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tsoka inu okhuta tsopano! cifukwa mudzamva njala, Tsoka inu, akuseka tsopano! cifukwa mudzacita maliro ndi kulira misozi.

Werengani mutu wathunthu Luka 6

Onani Luka 6:25 nkhani