Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Luka 5:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma kuti mudziwe kuti Mwana wa munthu ali nayo mphamvu pa dziko lapansi yakukhululukira macimo, (anati iye kwa wamanjenjeyo), Ndinena kwa iwe, Tauka, nusenze kama wako, numuke kunyumba kwako.

Werengani mutu wathunthu Luka 5

Onani Luka 5:24 nkhani