Ndipo anamtsogolera iye ku Yerusalemu, namuika iye pamwamba pa cimbudzi ca Kacisiyo, nati kwa iye, Ngati muli Mwana wa Mulungu, tadzigwetsani nokha pansi;