Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Luka 4:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iye anatsika nadza ku Kapernao, ndiwo mudzi wa ku Galileya, Ndipo analikuwaphunzitsa iwo pa Sabata; ndipo anadabwa ndi ciphunzitso cace;

Werengani mutu wathunthu Luka 4

Onani Luka 4:31 nkhani