Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Luka 4:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma zoonadi ndinena kwa inu, kuti, Munali akazi amasiye ambiri m'lsrayeli masiku ace a Eliya, pamene kunatsekedwa kumwamba zaka zitatu ndi miyezi isanu ndi umodzi, pamene panakhala njala yaikuru pa dziko lonselo;

Werengani mutu wathunthu Luka 4

Onani Luka 4:25 nkhani