Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Luka 4:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo m'mene iye anapinda bukulo, nalipereka kwa mnyamata, anakhala pansi; ndipo maso ao a anthu onse m'sunagogemo anamyang'anitsa iye.

Werengani mutu wathunthu Luka 4

Onani Luka 4:20 nkhani