Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Luka 4:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yesu, wodzala ndi Mzimu Woyera, anabwera kucokera ku Yordano, natsogozedwa ndi Mzimu kunka kucipululu kukayesedwa ndi mdierekezi masiku makumi anai.

Werengani mutu wathunthu Luka 4

Onani Luka 4:1 nkhani