Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Luka 3:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yohane anayankha, nanena kwa onse, Inetu ndikubatizani inu ndi madzi; koma wakundiposa ine mphamvu alinkudza, amene sindiyenera kumasula lamba la nsapato zace; Iyeyu adzakubatizani inu ndi Mzimu Woyera ndi moto:

Werengani mutu wathunthu Luka 3

Onani Luka 3:16 nkhani