Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Luka 3:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo asilikari omwe anamfunsa iye, nati, Nanga ife tizicita ciani? Ndipo iye anati kwa iwo, Musaopse, musanamize munthu ali yense; khalani okhuta ndi kulipira kwanu.

Werengani mutu wathunthu Luka 3

Onani Luka 3:14 nkhani