Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Luka 24:44 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anati kwa iwo, 5 Awa ndi mauwo ndinalankhula nanu, paja ndinakhala ndi inu, kuti ziyenera kukwanitsidwa zonse zolembedwa za Ine m'cilamulo ca 6 Mose, ndi aneneri, ndi masalmo.

Werengani mutu wathunthu Luka 24

Onani Luka 24:44 nkhani