Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Luka 24:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mmodzi wa iwo, dzina lace Kleopa, anayankha nati kwa iye, Kodi iwe wekha ndiwe mlendo m'Yerusalemu ndi wosazindikira zidacitikazi masiku omwe ano?

Werengani mutu wathunthu Luka 24

Onani Luka 24:18 nkhani