Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Luka 24:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Koma tsiku loyamba la sabata, mbanda kuca, anadza kumanda atatenga zonunkhira adazikonza.

2. Ndipo anapeza mwala unakunkhunizidwa kuucotsa pamanda.

3. Ndipo m'mene analowa sanapeza mtembo wa Ambuye Yesu.

Werengani mutu wathunthu Luka 24