Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Luka 23:44 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ora lace pamenepo linali ngati lacisanu ndi cimodzi. Ndipo panali mdima pa dziko lonse kufikira ora lacisanu ndi cinai, ndipo dzuwa linada.

Werengani mutu wathunthu Luka 23

Onani Luka 23:44 nkhani