Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Luka 23:39 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mmodzi wa ocita zoipa anapacikidwawo anamcitira iye mwano nanena, Kodi suli Kristu Iwe? udzipulumutse wekha ndi ife.

Werengani mutu wathunthu Luka 23

Onani Luka 23:39 nkhani