Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Luka 22:68-70 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

68. ndipo ndikakufunsani kanthu, simudzayankha.

69. Koma 15 kuyambira tsopano Mwana wa munthu adzakhala pa dzanja lamanja la mphamvu ya Mulungu.

70. Ndipo onse anati, Umo mtero, muli Mwana wa Mulungu kodi? Ndipo iye anati kwa iwo, 16 Munena kuti ndine.

Werengani mutu wathunthu Luka 22