Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Luka 22:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipo phwando la mikate yopanda cotupitsa linayandikira, ndilo lochedwa Paskha.

2. Ndipo ansembe akuru ndi alembi anafunafuna maphedwe ace pakuti anaopa anthuwoo.

3. Ndipo Satana analowa m'Yudase wonenedwa Isikariote, amene anawerengedwa mmodzi wa khumi ndi awiriwo,

Werengani mutu wathunthu Luka 22