Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Luka 21:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iye anati, Yang'anirani musasoceretsedwe; pakuti ambiri adzadza m'dzina langa, nadzanena, Ndine amene; ndipo, Nthawi yayandikira; musawatsate pambuyo pao.

Werengani mutu wathunthu Luka 21

Onani Luka 21:8 nkhani