Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Luka 21:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipo Yesu anakweza maso, naona anthu eni cuma alikuika zopereka zao mosungiramo ndalama.

2. Ndipo anaona mkazi wina wamasiye waumphawi alikuika momwemo timakobiri tiwiri.

Werengani mutu wathunthu Luka 21