Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Luka 2:48 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo m'mene anamuona iye, anadabwa; ndipo amace anati kwa iye, Mwanawe, wacitiranji ife cotero; taona, atate wako ndi ine tinalikufunafuna Iwe ndi kuda nkhawa.

Werengani mutu wathunthu Luka 2

Onani Luka 2:48 nkhani