Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Luka 19:34-36 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

34. Ndipo anati, Ambuye amfuna iye.

35. Ndipo anadzanave kwa Yesu; ndipo anayalika zobvala zao pa mwana wa buruyo, nakwezapo Yesu.

36. Ndipo pakupita iye, anayala zobvala zao m'njira.

Werengani mutu wathunthu Luka 19