Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Luka 19:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipo analowa, napyola pa Yeriko. Ndipo taonani, mwamuna wochedwa dzina lace Zakeyu;

2. ndipo Iye anali mkulu wa amisonkho, nali wacuma.

3. Ndipo anafuna kuona Yesu ndiye uti, ndipo sana the, cifukwa ca khamulo, pakuti anali wamfupi msinkhu.

Werengani mutu wathunthu Luka 19