Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Luka 18:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma m'mene Yesu anamva, anati kwa iye, Usowa cinthu cimodzi: gulitsa ziri zonse uli nazo, nugawire osauka; ndipo udzakhala naco cuma ceni ceni m'Mwamba; ndipo ukadze kuno, unditsate Ine.

Werengani mutu wathunthu Luka 18

Onani Luka 18:22 nkhani