Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Luka 17:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tsikulo iye amene adzakhala pamwamba pa chindwi, ndi akatundu ace m'nyumba, asatsike kuwatenga; ndipo iye amene ali m'munda modzimodzi asabwere ku zace za m'mbuyo.

Werengani mutu wathunthu Luka 17

Onani Luka 17:31 nkhani