Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Luka 16:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali kuti wopemphayo adafa, ndi kuti anatengedwa iye ndi angelo kunka ku cifuwa ca Abrahamu; ndipo mwini cumayo adafanso, naikidwa m'manda.

Werengani mutu wathunthu Luka 16

Onani Luka 16:22 nkhani