Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Luka 14:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ananenanso kwa iye amene adamuitana, Pamene ukonza cakudya ca pausana kapena ca madzulo, usaitane abwenzi ako, kapena abale ako, kapena a pfuko lako, kapena anansi ako eni cuma; kuti kapena iwonso angabwereze kuitana iwe, ndipo udzakhala nayo mphotho.

Werengani mutu wathunthu Luka 14

Onani Luka 14:12 nkhani