Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Luka 13:34 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yerusalemu, Yerusalemu, iwe wakupha aneneri, ndi wakuponya miyala iwo atumidwa kwa iwe! ha! kawiri kawiri ndinafuna kusonkhanitsa ana ako, monga ngati thadzi ndi anapiye ace m'mapiko ace, ndipo simunafunai!

Werengani mutu wathunthu Luka 13

Onani Luka 13:34 nkhani