Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Luka 13:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ufanana ndi kambeu kampiru, kamene munthu anatenga, nakaponya m'munda wace wace, ndipo kanamera, kanakula mtengo; ndi mbalame za m'mlengalenga zinabindikira mu nthambi zace.

Werengani mutu wathunthu Luka 13

Onani Luka 13:19 nkhani