Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Luka 13:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mkuru wa sunagoge anabvutika mtima, cifukwa Yesu anaciritsa tsiku la Sabata, nayankha, nanena kwa khamulo, Alipo masiku asanu ndi limodzi, m'menemo anthu ayenera kugwira nchito, cifukwa cace idzani kudzaciritsldwa momwemo, koma tsiku la Sabata ai.

Werengani mutu wathunthu Luka 13

Onani Luka 13:14 nkhani