Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Luka 13:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipo anakhalako nthawi yomweyo, anthu ena amene anamuuza iye za Agalileya, amene Pilato anasanganiza mwazi wao ndi nsembe zao.

2. Ndipo iye anayankha nati kwa iwo, Kodi muyesa kuti Agalileya aja anali anthu akucimwa koposa Agalileya onse, cifukwa anamva zowawa izi?

Werengani mutu wathunthu Luka 13