Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Luka 12:42 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Ambuye anati, Ndani tsono ali mdindo wokhulupirika ndi wanzeru, amene mbuye wace adzamuika kapitao wa pa banja lace, kuwapatsa iwo phoso lao pa nthawi yace?

Werengani mutu wathunthu Luka 12

Onani Luka 12:42 nkhani