Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Luka 11:42 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma tsoka inu, Afarisi! cifukwa mupereka limodzi la magawo khumi la timbeu tonunkhira, ndi timbeu tokometsa cakudya ndi ndiwo zonse, ndipo mumaleka ciweruziro ndi cikondi ca Mulungu; mwenzi mutacita izi, ndi kusasiya zinazo.

Werengani mutu wathunthu Luka 11

Onani Luka 11:42 nkhani