Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Luka 11:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma iye, podziwa zolingirira zao, anati kwa iwo, Ufumu uli wonse wogawanika m'kati mwace upasuka; ndipo nyumba ikagawanika m'kati mwace igwa.

Werengani mutu wathunthu Luka 11

Onani Luka 11:17 nkhani