Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Luka 1:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mngelo anayankha, nati kwa iye, ine ndine Gabrieli, woimirira pamaso pa Mulungu; ndipo ndinatumidwa kwa iwe kudzalankhula nawe, ndi kuuza iwe uthenga uwu wabwino.

Werengani mutu wathunthu Luka 1

Onani Luka 1:19 nkhani