Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Filemoni 1:8-10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

8. Momwemo, ndingakhale ndiri nako kulimbika mtima kwakukuru m'Kristu kukulamulira cimene ciyenera,

9. koma makamaka ndidandaulira mwa cikondi, pokhala wotere, Paulo nkhalamba, ndipo tsopano wandendenso wa Kristu Yesu;

10. ndikudandaulira cifukwa ca mwana wanga, amene ndambala m'ndende, Onesimo,

Werengani mutu wathunthu Filemoni 1