Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Filemoni 1:22-25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

22. Koma undikonzerenso pogona; pakuti ndiyembekeza kuti mwa mapemphero anu ndidzapatsidwa kwa inu.

23. Epafra wandende mnzanga mwa Kristu Yesu akulankhula iwe;

24. ateronso, Marko, Aristarko, Dema, Luka, anchito anzanga.

25. Cisomo ca Ambuye wathu Yesu Kristu cikhale pamodzi ndi mzimu wanu. Amen.

Werengani mutu wathunthu Filemoni 1